Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Kenako Yesuwa+ mwana wa Yehozadaki ndi ansembe anzake ndiponso Zerubabele+ mwana wa Salatiyeli+ ndi abale ake, anakamanga guwa lansembe la Mulungu wa Isiraeli. Anachita zimenezi kuti aziperekerapo nsembe zopsereza, mogwirizana ndi zimene zinalembedwa mʼChilamulo cha Mose,+ munthu wa Mulungu woona.

  • Nehemiya 12:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ansembe ndi Alevi amene anapita ndi Zerubabele+ mwana wa Salatiyeli+ ndi Yesuwa+ ndi awa: Seraya, Yeremiya, Ezara,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena