Mateyu 13:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Kodi uyu si mwana wa kalipentala uja?+ Kodi mayi ake si Mariya, ndipo azichimwene ake si Yakobo, Yosefe, Simoni ndi Yudasi?+ Maliko 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kodi iyeyu si kalipentala,+ mwana wa Mariya,+ komanso mchimwene wake wa Yakobo,+ Yosefe, Yudasi ndi Simoni?+ Ndipo azichemwali ake si awa tili nawo pompano?” Choncho anayamba kukhumudwa naye.
55 Kodi uyu si mwana wa kalipentala uja?+ Kodi mayi ake si Mariya, ndipo azichimwene ake si Yakobo, Yosefe, Simoni ndi Yudasi?+
3 Kodi iyeyu si kalipentala,+ mwana wa Mariya,+ komanso mchimwene wake wa Yakobo,+ Yosefe, Yudasi ndi Simoni?+ Ndipo azichemwali ake si awa tili nawo pompano?” Choncho anayamba kukhumudwa naye.