Yohane 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho Tomasi, amene ankadziwikanso kuti Didimo, anauza ophunzira anzakewo kuti: “Ifenso tiyeni tipite, kuti tikafere naye limodzi.”+ Yohane 20:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako anauza Tomasi kuti: “Ika chala chako apa ndiponso ona mʼmanja mwangamu. Bweretsa dzanja lako ugwire munthiti mwangamu ndipo usiye kukayikira* koma ukhulupirire.”
16 Choncho Tomasi, amene ankadziwikanso kuti Didimo, anauza ophunzira anzakewo kuti: “Ifenso tiyeni tipite, kuti tikafere naye limodzi.”+
27 Kenako anauza Tomasi kuti: “Ika chala chako apa ndiponso ona mʼmanja mwangamu. Bweretsa dzanja lako ugwire munthiti mwangamu ndipo usiye kukayikira* koma ukhulupirire.”