Yohane 14:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma mthandizi, amene ndi mzimu woyera umene Atate wanga adzatumize mʼdzina langa, adzakuphunzitsani komanso kukukumbutsani zinthu zonse zimene ndinakuuzani.+
26 Koma mthandizi, amene ndi mzimu woyera umene Atate wanga adzatumize mʼdzina langa, adzakuphunzitsani komanso kukukumbutsani zinthu zonse zimene ndinakuuzani.+