-
Luka 12:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Choncho chilichonse chimene mumanena mumdima chidzamveka poyera ndipo zimene mumanongʼona kwanokha mʼzipinda zanu zidzalalikidwa padenga.
-