Mateyu 25:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Koma poyankha Mfumuyo idzawauza kuti, ‘Ndithu ndikukuuzani, nthawi iliyonse imene munachitira zimenezo mmodzi wa abale anga aangʼono awa, munachitiranso ine.’+ Luka 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Amene akukumverani, akumveranso ine.+ Amene akunyalanyaza inu, akunyalanyazanso ine ndipo amene akunyalanyaza ine, akunyalanyazanso Mulungu amene anandituma.”+ Yohane 12:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Koma Yesu anafuula kuti: “Aliyense amene akukhulupirira ine sakukhulupirira ine ndekha, koma akukhulupiriranso amene anandituma.+ Yohane 13:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndithudi ndikukuuzani, aliyense amene walandira yemwe ine ndamutuma walandiranso ine.+ Ndipo amene walandira ine, walandiranso amene anandituma.”+
40 Koma poyankha Mfumuyo idzawauza kuti, ‘Ndithu ndikukuuzani, nthawi iliyonse imene munachitira zimenezo mmodzi wa abale anga aangʼono awa, munachitiranso ine.’+
16 Amene akukumverani, akumveranso ine.+ Amene akunyalanyaza inu, akunyalanyazanso ine ndipo amene akunyalanyaza ine, akunyalanyazanso Mulungu amene anandituma.”+
44 Koma Yesu anafuula kuti: “Aliyense amene akukhulupirira ine sakukhulupirira ine ndekha, koma akukhulupiriranso amene anandituma.+
20 Ndithudi ndikukuuzani, aliyense amene walandira yemwe ine ndamutuma walandiranso ine.+ Ndipo amene walandira ine, walandiranso amene anandituma.”+