Luka 16:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Anthu ankalalikira za Chilamulo ndi zimene aneneri analemba kudzafika mʼnthawi ya Yohane. Kuyambira nthawi imeneyo, uthenga wabwino umene ukulengezedwa ndi wokhudza Ufumu wa Mulungu, ndipo anthu osiyanasiyana akuyesetsa mwakhama kuti akalowemo.+
16 Anthu ankalalikira za Chilamulo ndi zimene aneneri analemba kudzafika mʼnthawi ya Yohane. Kuyambira nthawi imeneyo, uthenga wabwino umene ukulengezedwa ndi wokhudza Ufumu wa Mulungu, ndipo anthu osiyanasiyana akuyesetsa mwakhama kuti akalowemo.+