Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Hoseya 6:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Chifukwa ndimakondwera ndi chikondi chokhulupirika,* osati nsembe.

      Ndimakondweranso ndi kudziwa Mulungu, osati nsembe zopsereza zathunthu.+

  • Mika 6:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Kodi nditenge chiyani popita kwa Yehova?

      Ndikagwade ndi chiyani kwa Mulungu wakumwamba?

      Kodi ndipite nditatenga nsembe zopsereza zathunthu?

      Ndiponso ana a ngʼombe achaka chimodzi?+

  • Mika 6:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Iye anakuuza munthu iwe zimene zili zabwino.

      Kodi Yehova akufuna kuti uzichita* chiyani?

      Iye akungofuna kuti uzichita chilungamo,*+ uziona kuti kukhulupirika nʼkofunika,*+

      Ndiponso uziyenda modzichepetsa+ ndi Mulungu wako.+

  • Mateyu 9:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Choncho pitani mukaphunzire tanthauzo la mawu akuti: ‘Ndikufuna chifundo, osati nsembe.’+ Chifukwa ine sindinabwere kudzaitana anthu olungama, koma ochimwa.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena