Maliko 2:27, 28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako anawauza kuti: “Sabata linakhalako chifukwa cha munthu,+ osati munthu chifukwa cha Sabata. 28 Choncho Mwana wa munthu ndi Mbuye wa Sabata.”+ Luka 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako anapitiriza kuwauza kuti: “Mwana wa munthu ndi Mbuye wa Sabata.”+
27 Kenako anawauza kuti: “Sabata linakhalako chifukwa cha munthu,+ osati munthu chifukwa cha Sabata. 28 Choncho Mwana wa munthu ndi Mbuye wa Sabata.”+