-
Mateyu 8:3, 4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Choncho Yesu anatambasula dzanja lake nʼkumukhudza ndipo ananena kuti: “Inde ndikufuna. Khala woyera.”+ Nthawi yomweyo khate lakelo linatha.+ 4 Ndiyeno Yesu anamuuza kuti: “Samala, usauze aliyense zimenezi,+ koma upite ukadzionetse kwa wansembe+ ndipo ukapereke mphatso imene Mose analamula,+ kuti ikhale umboni kwa iwo.”
-