Mateyu 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yohane ataona Afarisi ndi Asaduki+ ambiri akubwera ku ubatizowo, anawauza kuti: “Ana a njoka inu,+ ndi ndani wakuchenjezani kuti muthawe mkwiyo umene ukubwerawo?+ Mateyu 23:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Njoka inu, ana a mphiri,+ mudzathawa bwanji chiweruzo cha Gehena?*+
7 Yohane ataona Afarisi ndi Asaduki+ ambiri akubwera ku ubatizowo, anawauza kuti: “Ana a njoka inu,+ ndi ndani wakuchenjezani kuti muthawe mkwiyo umene ukubwerawo?+