Maliko 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho mbewu zimene zimagwera mʼmbali mwa msewu ndi mawu amene afesedwa mwa anthu amene amati akangomva mawuwo, Satana amabwera+ nʼkudzachotsa mawu amene afesedwa mwa iwo.+ Luka 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Zogwera mʼmbali mwa msewuzo ndi anthu amene amamva mawuwo. Kenako Mdyerekezi amabwera nʼkudzachotsa mawuwo mʼmitima yawo kuti asakhulupirire ndiponso kupulumuka.+
15 Choncho mbewu zimene zimagwera mʼmbali mwa msewu ndi mawu amene afesedwa mwa anthu amene amati akangomva mawuwo, Satana amabwera+ nʼkudzachotsa mawu amene afesedwa mwa iwo.+
12 Zogwera mʼmbali mwa msewuzo ndi anthu amene amamva mawuwo. Kenako Mdyerekezi amabwera nʼkudzachotsa mawuwo mʼmitima yawo kuti asakhulupirire ndiponso kupulumuka.+