Maliko 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pomaliza, mbewu zimene zinafesedwa panthaka yabwino ndi anthu amene amamvetsera mawu ndipo amawalandira bwino nʼkubereka zipatso wina 30, wina 60 ndipo wina 100.”+ Luka 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma zogwera panthaka yabwino, ndi anthu amene pambuyo pomva mawuwo ndi mtima wabwino kwambiri,+ amawagwiritsitsa nʼkubereka zipatso mopirira.+
20 Pomaliza, mbewu zimene zinafesedwa panthaka yabwino ndi anthu amene amamvetsera mawu ndipo amawalandira bwino nʼkubereka zipatso wina 30, wina 60 ndipo wina 100.”+
15 Koma zogwera panthaka yabwino, ndi anthu amene pambuyo pomva mawuwo ndi mtima wabwino kwambiri,+ amawagwiritsitsa nʼkubereka zipatso mopirira.+