Mateyu 13:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Zisiyeni zonse zikulire limodzi mpaka nthawi yokolola. Mʼnyengo yokolola ndidzauza okolola kuti: Choyamba sonkhanitsani namsongole nʼkumumanga mʼmitolo kuti akawotchedwe. Kenako musonkhanitse tirigu mʼnyumba yanga yosungiramo zinthu.’”+
30 Zisiyeni zonse zikulire limodzi mpaka nthawi yokolola. Mʼnyengo yokolola ndidzauza okolola kuti: Choyamba sonkhanitsani namsongole nʼkumumanga mʼmitolo kuti akawotchedwe. Kenako musonkhanitse tirigu mʼnyumba yanga yosungiramo zinthu.’”+