Oweruza 5:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Inu Yehova, adani anu onse afafanizidwe,+Koma amene amakukondani awale ngati mmene dzuwa limawalira likamatuluka.” Ndipo dzikolo linakhala pa mtendere kwa zaka 40.+
31 Inu Yehova, adani anu onse afafanizidwe,+Koma amene amakukondani awale ngati mmene dzuwa limawalira likamatuluka.” Ndipo dzikolo linakhala pa mtendere kwa zaka 40.+