Mateyu 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atafika kumeneko anakakhala mumzinda wotchedwa Nazareti+ kuti akwaniritse mawu amene Mulungu ananena kudzera mwa aneneri kuti: “Iye adzatchedwa Mnazareti.”*+
23 Atafika kumeneko anakakhala mumzinda wotchedwa Nazareti+ kuti akwaniritse mawu amene Mulungu ananena kudzera mwa aneneri kuti: “Iye adzatchedwa Mnazareti.”*+