-
Genesis 38:29, 30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Koma mwanayo anabweza dzanja lake. Nthawi yomweyo mchimwene wake anatuluka, moti mzambayo anafuula kuti: “Bwanji ukuchita kungʼamba njira?” Nʼchifukwa chake anamupatsa dzina lakuti Perezi.*+ 30 Pambuyo pake, mʼbale wake yemwe anali ndi kachingwe kofiira padzanja lake uja anatuluka, ndipo anamupatsa dzina lakuti Zera.+
-