Luka 11:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Koma Mfarisiyo anadabwa ataona kuti akudya chakudyacho asanasambe.*+ Yohane 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamalopo panali mbiya zamiyala zokwana 6, mogwirizana ndi malamulo a Ayuda a kudziyeretsa.+ Mbiya iliyonse inali ya malita pafupifupi 44 mpaka 66.*
6 Pamalopo panali mbiya zamiyala zokwana 6, mogwirizana ndi malamulo a Ayuda a kudziyeretsa.+ Mbiya iliyonse inali ya malita pafupifupi 44 mpaka 66.*