-
Mateyu 23:15, 16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Tsoka kwa inu alembi ndi Afarisi, anthu achinyengo inu!+ Chifukwa mumawoloka nyanja komanso kuyenda mitunda italiitali kuti mukatembenuze munthu mmodzi. Koma akatembenuka mumamupangitsa kuti akhale woyenera kuponyedwa mʼGehena* kuposa inuyo.
16 Tsoka kwa inu atsogoleri akhungu,+ amene mumati, ‘Ngati munthu watchula kachisi polumbira, palibe kanthu, koma ngati munthu watchula golide wa mʼkachisi, akuyenera kusunga lumbiro lake.’+
-