Mateyu 9:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Atatulutsa chiwandacho, munthu wosalankhulayo analankhula,+ moti gulu la anthulo linadabwa ndipo linanena kuti: “Zoterezi sizinaonekepo nʼkale lonse mu Isiraeli.”+
33 Atatulutsa chiwandacho, munthu wosalankhulayo analankhula,+ moti gulu la anthulo linadabwa ndipo linanena kuti: “Zoterezi sizinaonekepo nʼkale lonse mu Isiraeli.”+