Mateyu 14:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yesu atatsika mʼngalawayo anaona gulu lalikulu la anthu ndipo anawamvera chisoni+ nʼkuwachiritsira anthu awo odwala.+ Maliko 6:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Koma atatsika anaona gulu lalikulu la anthu ndipo anawamvera chisoni,+ chifukwa anali ngati nkhosa zimene zilibe mʼbusa.+ Ndiye anayamba kuwaphunzitsa zinthu zambiri.+
14 Yesu atatsika mʼngalawayo anaona gulu lalikulu la anthu ndipo anawamvera chisoni+ nʼkuwachiritsira anthu awo odwala.+
34 Koma atatsika anaona gulu lalikulu la anthu ndipo anawamvera chisoni,+ chifukwa anali ngati nkhosa zimene zilibe mʼbusa.+ Ndiye anayamba kuwaphunzitsa zinthu zambiri.+