Levitiko 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Usamadane ndi mʼbale wako mumtima mwako,+ koma uzimudzudzula+ kuti iwenso usakhale wochimwa ngati iyeyo. Miyambo 25:8, 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Usamafulumire kupititsa mlandu kukhoti,Chifukwa udzachita chiyani mnzako akadzapereka umboni wosonyeza kuti iweyo ndi wolakwa?+ 9 Thetsa nkhaniyo pokambirana ndi mnzakoyo,+Koma usaulule nkhani zachinsinsi zimene unauzidwa,*+ Luka 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Samalani ndithu. Ngati mʼbale wako wachita tchimo umudzudzule+ ndipo akalapa umukhululukire.+
17 Usamadane ndi mʼbale wako mumtima mwako,+ koma uzimudzudzula+ kuti iwenso usakhale wochimwa ngati iyeyo.
8 Usamafulumire kupititsa mlandu kukhoti,Chifukwa udzachita chiyani mnzako akadzapereka umboni wosonyeza kuti iweyo ndi wolakwa?+ 9 Thetsa nkhaniyo pokambirana ndi mnzakoyo,+Koma usaulule nkhani zachinsinsi zimene unauzidwa,*+ Luka 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Samalani ndithu. Ngati mʼbale wako wachita tchimo umudzudzule+ ndipo akalapa umukhululukire.+