Yohane 18:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno iwo anatenga Yesu kuchoka kwa Kayafa nʼkupita naye kunyumba ya bwanamkubwa.+ Umenewu unali mʼmawa kwambiri. Koma iwo sanalowe mʼnyumba ya bwanamkubwayo poopa kudetsedwa.+ Iwo ankafuna kuti akathe kudya Pasika. Machitidwe 10:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno Petulo anawauza kuti: “Inunso mukudziwa bwino kuti si zololeka kuti Myuda azicheza ndi munthu wa mtundu wina kapena kumuyandikira.+ Koma Mulungu wandionetsa kuti ndisatchule munthu aliyense kuti wodetsedwa kapena wonyansa.+ Machitidwe 11:2, 3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma Petulo atapita ku Yerusalemu, anthu olimbikitsa mdulidwe+ anayamba kumuimba mlandu. 3 Iwo ankamunena kuti: “Iwe unakalowa mʼnyumba ya anthu osadulidwa ndipo unadya nawo.”
28 Ndiyeno iwo anatenga Yesu kuchoka kwa Kayafa nʼkupita naye kunyumba ya bwanamkubwa.+ Umenewu unali mʼmawa kwambiri. Koma iwo sanalowe mʼnyumba ya bwanamkubwayo poopa kudetsedwa.+ Iwo ankafuna kuti akathe kudya Pasika.
28 Ndiyeno Petulo anawauza kuti: “Inunso mukudziwa bwino kuti si zololeka kuti Myuda azicheza ndi munthu wa mtundu wina kapena kumuyandikira.+ Koma Mulungu wandionetsa kuti ndisatchule munthu aliyense kuti wodetsedwa kapena wonyansa.+
2 Koma Petulo atapita ku Yerusalemu, anthu olimbikitsa mdulidwe+ anayamba kumuimba mlandu. 3 Iwo ankamunena kuti: “Iwe unakalowa mʼnyumba ya anthu osadulidwa ndipo unadya nawo.”