-
Yesaya 53:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Chifukwa cha kuvutika kwake, iye adzaona zabwino ndipo adzakhutira.
-
-
Tito 2:13, 14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 pamene tikuyembekezera zinthu zosangalatsa+ ndiponso kuonekera kwaulemerero kwa Mulungu wamkulu komanso kwa Mpulumutsi wathu, Yesu Khristu, 14 amene anadzipereka mʼmalo mwa ife+ kuti atilanditse*+ ku moyo wochita zinthu zosamvera malamulo za mtundu uliwonse ndiponso kuti atiyeretse, kuti tikhale anthu ake apadera, odzipereka pa ntchito zabwino.+
-