Yesaya 62:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Taonani! Yehova walengeza mpaka kumalekezero a dziko lapansi kuti: “Mwana wamkazi wa Ziyoni* mumuuze kuti,‘Taona! Chipulumutso chako chikubwera.+ Taona! Mphoto yake ili ndi iyeyo,Ndipo malipiro amene amapereka ali pamaso pake.’”+ Yohane 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Usaope mwana wamkazi wa Ziyoni. Taona! Mfumu yako ikubwera itakwera mwana wamphongo wa bulu.”+
11 Taonani! Yehova walengeza mpaka kumalekezero a dziko lapansi kuti: “Mwana wamkazi wa Ziyoni* mumuuze kuti,‘Taona! Chipulumutso chako chikubwera.+ Taona! Mphoto yake ili ndi iyeyo,Ndipo malipiro amene amapereka ali pamaso pake.’”+