Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 7:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Kodi nyumba iyi, imene imatchedwa ndi dzina langa, mwayamba kuiona ngati phanga la achifwamba?+ Inetu ndaona zimene mukuchita,” akutero Yehova.

  • Maliko 11:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Iye ankaphunzitsa ndipo ankauza anthuwo kuti: “Kodi Malemba sanena kuti, ‘Nyumba yanga idzatchedwa nyumba yopemphereramo anthu a mitundu yonseʼ?+ Koma inu mwaisandutsa phanga la achifwamba.”+

  • Luka 19:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 nʼkuwauza kuti: “Malemba amati, ‘Nyumba yanga idzakhala nyumba yopemphereramo,’+ koma inu mwaisandutsa phanga la achifwamba.”+

  • Yohane 2:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndiyeno anauza ogulitsa nkhundawo kuti: “Chotsani izi muno! Musiyiretu kusandutsa nyumba ya Atate wanga kukhala nyumba ya malonda!”*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena