Maliko 11:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ansembe aakulu ndi alembi anamva zimenezo, ndipo anayamba kufunafuna njira yoti amuphere+ chifukwa ankamuopa popeza gulu lonse la anthu linkadabwa ndi zimene ankaphunzitsa.+ Luka 19:39, 40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Koma Afarisi ena mʼgululo anauza Yesu kuti: “Mphunzitsi, adzudzuleni ophunzira anuwa.”+ 40 Poyankha iye anati: “Ndithu ndikukuuzani, ngati awa atakhala chete, miyala ingathe kufuula.”
18 Ansembe aakulu ndi alembi anamva zimenezo, ndipo anayamba kufunafuna njira yoti amuphere+ chifukwa ankamuopa popeza gulu lonse la anthu linkadabwa ndi zimene ankaphunzitsa.+
39 Koma Afarisi ena mʼgululo anauza Yesu kuti: “Mphunzitsi, adzudzuleni ophunzira anuwa.”+ 40 Poyankha iye anati: “Ndithu ndikukuuzani, ngati awa atakhala chete, miyala ingathe kufuula.”