Salimo 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kudzera mʼmawu otamanda ochokera mʼkamwa mwa ana ndi mwa makanda+Mwasonyeza mphamvu zanu chifukwa cha adani anu,Kuti adani anu komanso amene akufuna kukubwezerani zoipa akhale chete.
2 Kudzera mʼmawu otamanda ochokera mʼkamwa mwa ana ndi mwa makanda+Mwasonyeza mphamvu zanu chifukwa cha adani anu,Kuti adani anu komanso amene akufuna kukubwezerani zoipa akhale chete.