Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 3:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Nkhwangwa yaikidwa kale pamizu yamitengo. Choncho mtengo uliwonse wosabereka zipatso zabwino udulidwa nʼkuponyedwa pamoto.+

  • Maliko 11:13, 14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndiye ali chapatali ndithu, anaona mtengo wamkuyu umene unali ndi masamba. Iye anapita pomwepo kuti akaone ngati angapezemo kanthu. Koma atafika pamtengowo, sanapezemo chilichonse koma masamba okha basi, chifukwa sinali nyengo ya nkhuyu. 14 Choncho iye anauza mtengowo kuti: “Munthu sadzadyanso zipatso zako mpaka kalekale.”+ Ndipo ophunzira ake ankamvetsera.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena