Aheberi 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kumapeto kwa masiku ano, iye walankhula ndi ife kudzera mwa Mwana wake,+ amene anamusankha kuti akhale wolandira zinthu zonse monga cholowa.+ Komanso kudzera mwa iyeyu, Mulungu anachititsa kuti pakhale nthawi* zosiyanasiyana.+
2 Kumapeto kwa masiku ano, iye walankhula ndi ife kudzera mwa Mwana wake,+ amene anamusankha kuti akhale wolandira zinthu zonse monga cholowa.+ Komanso kudzera mwa iyeyu, Mulungu anachititsa kuti pakhale nthawi* zosiyanasiyana.+