Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 4:1, 2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pamene Petulo ndi Yohane ankalankhula ndi anthuwo, ansembe, woyangʼanira kachisi ndiponso Asaduki+ anafika. 2 Iwo anakwiya chifukwa atumwiwo ankaphunzitsa anthu ndiponso kulalikira mosapita mʼmbali zoti Yesu anaukitsidwa.+

  • Machitidwe 23:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Chifukwa Asaduki amanena kuti munthu wakufa sangauke komanso kulibe angelo kapena cholengedwa chauzimu. Pomwe Afarisi amavomereza poyera kuti zonsezi zilipo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena