Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 38:7, 8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Koma makhalidwe a Ere, mwana woyamba wa Yuda, sanasangalatse Yehova ndipo Yehova anamupha. 8 Yuda ataona zimenezi anauza Onani kuti: “Gona ndi mkazi wa mchimwene wako ndipo ulowe chokolo,* kuti umuberekere ana mchimwene wako.”+

  • Deuteronomo 25:5, 6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ngati amuna apachibale akukhala moyandikana, ndiyeno mmodzi nʼkumwalira asanabereke mwana wamwamuna, mkazi wa womwalirayo asakwatiwe ndi mwamuna wochokera mʼbanja lina. Mlamu wake azipita kwa iye nʼkukamutenga kukhala mkazi wake, ndipo azichita ukwati wa pachilamu.+ 6 Mwana woyamba amene mkaziyo angabereke, azitenga dzina la mwamuna womwalira uja,+ kuti dzina la mʼbale wake lisathe mu Isiraeli.+

  • Rute 1:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Koma Naomi anati: “Bwererani ana anga. Palibe chifukwa choti tipitire limodzi. Kodi ndingathe kuberekanso ana amene angadzakhale amuna anu?+

  • Rute 3:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Gona pompano lero. Ngati iye angakuwombole mawa, zili bwino akuwombole.+ Koma ngati sakufuna kukuwombola, ineyo ndikuwombola. Ndithudi, pali Yehova Mulungu wamoyo, ndikuwombola. Gona mpaka mʼmawa.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena