Maliko 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Komanso mukadzamva phokoso la nkhondo ndi malipoti a nkhondo, musadzachite mantha. Zimenezi zikuyenera kuchitika ndithu, koma mapeto adzakhala asanafikebe.+ Luka 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Komanso, mukadzamva phokoso la nkhondo ndi zipolowe,* musadzachite mantha. Chifukwa zimenezi zikuyenera kuchitika choyamba, koma mapeto sadzafika nthawi yomweyo.”+
7 Komanso mukadzamva phokoso la nkhondo ndi malipoti a nkhondo, musadzachite mantha. Zimenezi zikuyenera kuchitika ndithu, koma mapeto adzakhala asanafikebe.+
9 Komanso, mukadzamva phokoso la nkhondo ndi zipolowe,* musadzachite mantha. Chifukwa zimenezi zikuyenera kuchitika choyamba, koma mapeto sadzafika nthawi yomweyo.”+