Chivumbulutso 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Taonani! Akubwera ndi mitambo+ ndipo diso lililonse lidzamuona, ngakhalenso anthu amene anamubaya. Ndipo mafuko onse apadziko lapansi adzadziguguda pachifuwa pomva chisoni chifukwa cha iye.+ Inde, zimenezi zidzachitikadi. Ame.
7 Taonani! Akubwera ndi mitambo+ ndipo diso lililonse lidzamuona, ngakhalenso anthu amene anamubaya. Ndipo mafuko onse apadziko lapansi adzadziguguda pachifuwa pomva chisoni chifukwa cha iye.+ Inde, zimenezi zidzachitikadi. Ame.