1 Atesalonika 5:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma tsopano za nthawi ndi nyengo abale, simukufunika kuti tikulembereni chilichonse. 2 Chifukwa inuyo mukudziwa bwino kuti tsiku la Yehova*+ lidzabwera ndendende ngati wakuba usiku.+
5 Koma tsopano za nthawi ndi nyengo abale, simukufunika kuti tikulembereni chilichonse. 2 Chifukwa inuyo mukudziwa bwino kuti tsiku la Yehova*+ lidzabwera ndendende ngati wakuba usiku.+