Aheberi 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chifukwa mkulu wa ansembe amene tili nayeyu, si mkulu wa ansembe amene sangatimvere chisoni pa zofooka zathu.+ Koma ndi mkulu wa ansembe amene anayesedwa pa zinthu zonse ngati ifeyo, ndipo anakhalabe wopanda uchimo.+
15 Chifukwa mkulu wa ansembe amene tili nayeyu, si mkulu wa ansembe amene sangatimvere chisoni pa zofooka zathu.+ Koma ndi mkulu wa ansembe amene anayesedwa pa zinthu zonse ngati ifeyo, ndipo anakhalabe wopanda uchimo.+