Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 7:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Choncho chigumulacho chisanayambe, Nowa analowa mʼchingalawacho, limodzi ndi ana ake aamuna, mkazi wake ndi akazi a ana ake.+

  • Aheberi 11:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Chifukwa cha chikhulupiriro, Nowa+ atachenjezedwa ndi Mulungu za zinthu zimene zinali zisanaoneke,+ anasonyeza kuopa Mulungu ndipo anamanga chingalawa+ kuti banja lake lipulumukiremo. Chifukwa cha chikhulupiriro, anatsutsa dziko+ ndipo anaonedwa kuti ndi wolungama chifukwa cha chikhulupirirocho.

  • 1 Petulo 3:19, 20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Kenako anapita kukalengeza uthenga wachiweruzo* kwa mizimu imene inali mʼndende.+ 20 Mizimuyi sinamvere Mulungu pa nthawi imene ankaleza mtima mʼmasiku a Nowa.+ Pa nthawiyo, Nowa ankapanga chingalawa+ chomwe chinapulumutsa pamadzi anthu owerengeka, anthu* 8 okha basi.+

  • 2 Petulo 2:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Mulungu sanalekerere dziko lakale lija osalipatsa chilango,+ koma anasunga Nowa, yemwe ankalalikira za chilungamo cha Mulungu.+ Anamupulumutsa limodzi ndi anthu enanso 7,+ pamene anabweretsa chigumula padziko la anthu osaopa Mulungu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena