Mateyu 25:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho pitirizani kukhala maso+ chifukwa simukudziwa tsiku kapena ola lake.+ Maliko 13:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Khalani maso, khalani tcheru,+ chifukwa simukudziwa kuti nthawi yoikidwiratu idzafika liti.+ Luka 21:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Choncho khalani maso+ ndipo muzipemphera mopembedzera nthawi zonse,+ kuti mudzathe kuthawa zinthu zonsezi zimene zikuyenera kuchitika, komanso kuti mudzathe kuima pamaso pa Mwana wa munthu.”+
36 Choncho khalani maso+ ndipo muzipemphera mopembedzera nthawi zonse,+ kuti mudzathe kuthawa zinthu zonsezi zimene zikuyenera kuchitika, komanso kuti mudzathe kuima pamaso pa Mwana wa munthu.”+