Chivumbulutso 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Taona! Ndikubwera ngati wakuba.+ Wosangalala ndi amene akukhalabe maso+ ndiponso amene wavalabe malaya ake akunja, kuti asayende wosavala anthu nʼkuona maliseche ake.”+
15 “Taona! Ndikubwera ngati wakuba.+ Wosangalala ndi amene akukhalabe maso+ ndiponso amene wavalabe malaya ake akunja, kuti asayende wosavala anthu nʼkuona maliseche ake.”+