1 Atesalonika 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nʼchifukwa chake pamene sindinathenso kupirira, ndinatuma Timoteyo kwa inu kuti ndidziwe za kukhulupirika kwanu.+ Ndimadera nkhawa kuti mwina Woyesayo+ anakuyesani ndipo nʼkutheka kuti ntchito imene tinagwira mwakhama inangopita pachabe.
5 Nʼchifukwa chake pamene sindinathenso kupirira, ndinatuma Timoteyo kwa inu kuti ndidziwe za kukhulupirika kwanu.+ Ndimadera nkhawa kuti mwina Woyesayo+ anakuyesani ndipo nʼkutheka kuti ntchito imene tinagwira mwakhama inangopita pachabe.