Ekisodo 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mʼmwezi woyamba, tsiku la 14 la mwezi umenewo, madzulo muzidzadya mikate yopanda zofufumitsa, mpaka kukafika madzulo a tsiku la 21 mwezi womwewo.+ Ekisodo 23:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Muzichita Chikondwerero cha Mikate Yopanda Zofufumitsa.+ Muzidya mikate yopanda zofufumitsa masiku 7 pa nthawi imene inaikidwa mʼmwezi wa Abibu*+ mogwirizana ndi zimene ndinakulamulani, chifukwa munatuluka mu Iguputo mʼmwezi umenewu. Ndipo palibe amene ayenera kuonekera kwa ine chimanjamanja.+ Luka 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tsopano Chikondwerero cha Mikate Yopanda Zofufumitsa, chimene chinkadziwikanso kuti Pasika,+ chinali chitayandikira.+
18 Mʼmwezi woyamba, tsiku la 14 la mwezi umenewo, madzulo muzidzadya mikate yopanda zofufumitsa, mpaka kukafika madzulo a tsiku la 21 mwezi womwewo.+
15 Muzichita Chikondwerero cha Mikate Yopanda Zofufumitsa.+ Muzidya mikate yopanda zofufumitsa masiku 7 pa nthawi imene inaikidwa mʼmwezi wa Abibu*+ mogwirizana ndi zimene ndinakulamulani, chifukwa munatuluka mu Iguputo mʼmwezi umenewu. Ndipo palibe amene ayenera kuonekera kwa ine chimanjamanja.+
22 Tsopano Chikondwerero cha Mikate Yopanda Zofufumitsa, chimene chinkadziwikanso kuti Pasika,+ chinali chitayandikira.+