Salimo 27:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Musandipereke kwa adani anga,+Chifukwa mboni zabodza zikundinamizira mlandu,+Ndipo akundiopseza kuti andichitira zachiwawa. Salimo 35:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mboni zoipa mtima zabwera,+Ndipo zikundifunsa zinthu zimene sindikuzidziwa.
12 Musandipereke kwa adani anga,+Chifukwa mboni zabodza zikundinamizira mlandu,+Ndipo akundiopseza kuti andichitira zachiwawa.