Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 22:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Iwo akugawana zovala zanga,

      Ndipo akuchita maere pa zovala zanga.+

  • Maliko 15:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Ndipo anamukhomerera pamtengo nʼkugawana malaya ake akunja pochita maere pa malayawo, kuti aone chimene munthu aliyense angatenge.+

  • Luka 23:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Koma Yesu ananena kuti: “Atate, akhululukireni, chifukwa sakudziwa zimene akuchita.” Iwo anagawana zovala zake pochita maere.+

  • Yohane 19:23, 24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Asilikaliwo atamukhomerera Yesu pamtengo, anatenga malaya ake akunja nʼkuwagawa zigawo 4, kuti msilikali aliyense atenge chigawo chimodzi. Anatenganso malaya amkati. Koma malaya amkatiwo analibe msoko, anawombedwa kuchokera pamwamba mpaka pansi. 24 Choncho iwo anakambirana kuti: “Malayawa tisawangʼambe, koma tiyeni tichite maere kuti tidziwe amene angatenge malaya amenewa.”+ Zimenezi zinachitika kuti lemba likwaniritsidwe, limene limati: “Iwo anagawana zovala zanga, ndipo anachita maere pa zovala zanga.”+ Choncho asilikaliwo anachitadi zimenezi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena