Salimo 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu onse amene amandiona amandiseka.+Iwo amandinyogodola nʼkumapukusa mitu yawo mondinyoza nʼkumati:+ Salimo 109:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Iwo akumandinyoza.+ Akandiona akumapukusa mitu yawo.+
7 Anthu onse amene amandiona amandiseka.+Iwo amandinyogodola nʼkumapukusa mitu yawo mondinyoza nʼkumati:+