Maliko 14:62 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Ndiyeno Yesu ananena kuti: “Inde ndinedi, ndipo mudzaona Mwana wa munthu+ atakhala kudzanja lamanja+ lamphamvu. Mudzamuonanso akubwera ndi mitambo yakumwamba.”+ Yohane 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pa chifukwa chimenechi Ayudawo anayamba kufunafuna njira yoti amuphere, chifukwa kuwonjezera pa kuphwanya Sabata, ankanenanso kuti Mulungu ndi Atate wake,+ kudziyesa wofanana ndi Mulungu.+ Yohane 10:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 kodi inu mukundiuza ine amene Atate anandiyeretsa nʼkunditumiza mʼdziko kuti, ‘Ukunyoza Mulungu,’ chifukwa ndanena kuti, ‘Ndine Mwana wa Mulunguʼ?+
62 Ndiyeno Yesu ananena kuti: “Inde ndinedi, ndipo mudzaona Mwana wa munthu+ atakhala kudzanja lamanja+ lamphamvu. Mudzamuonanso akubwera ndi mitambo yakumwamba.”+
18 Pa chifukwa chimenechi Ayudawo anayamba kufunafuna njira yoti amuphere, chifukwa kuwonjezera pa kuphwanya Sabata, ankanenanso kuti Mulungu ndi Atate wake,+ kudziyesa wofanana ndi Mulungu.+
36 kodi inu mukundiuza ine amene Atate anandiyeretsa nʼkunditumiza mʼdziko kuti, ‘Ukunyoza Mulungu,’ chifukwa ndanena kuti, ‘Ndine Mwana wa Mulunguʼ?+