Maliko 15:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Tsopano, mtsogoleri wa asilikali amene anaimirira chapafupi moyangʼanizana ndi Yesu, ataona zimene zinachitika pa nthawi imene anatsirizika, ananena kuti: “Ndithudi munthu uyu analidi Mwana wa Mulungu.”+
39 Tsopano, mtsogoleri wa asilikali amene anaimirira chapafupi moyangʼanizana ndi Yesu, ataona zimene zinachitika pa nthawi imene anatsirizika, ananena kuti: “Ndithudi munthu uyu analidi Mwana wa Mulungu.”+