Mateyu 20:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako mkazi wa Zebedayo+ anafika kwa Yesu ndi ana ake aamuna ndipo anamugwadira nʼkumupempha kanthu kena.+ Yohane 19:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma chapafupi ndi mtengo wozunzikirapo* wa Yesu, panaima mayi ake+ ndi mchemwali wa mayi akewo, Mariya mkazi wa Kulopa, komanso Mariya wa ku Magadala.+
20 Kenako mkazi wa Zebedayo+ anafika kwa Yesu ndi ana ake aamuna ndipo anamugwadira nʼkumupempha kanthu kena.+
25 Koma chapafupi ndi mtengo wozunzikirapo* wa Yesu, panaima mayi ake+ ndi mchemwali wa mayi akewo, Mariya mkazi wa Kulopa, komanso Mariya wa ku Magadala.+