Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Maliko 16:4, 5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Koma atayangʼanitsitsa, anaona kuti mwalawo wagubuduzidwa kale ngakhale kuti unali waukulu kwambiri.+ 5 Atalowa mʼmandamo, anaona mnyamata atakhala pansi mbali yakumanja, atavala mkanjo woyera ndipo iwo anadabwa kwambiri.

  • Luka 24:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Koma anapeza kuti mwala wagubuduzidwa pamandawo,*+

  • Luka 24:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Atathedwa nzeru ndi zimenezi, anangoona amuna awiri ovala zovala zonyezimira ataima pambali pawo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena