Mateyu 26:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Koma ndikadzauka kwa akufa, ndidzatsogola kukafika ku Galileya inu musanafikeko.”+ Mateyu 28:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma ophunzira 11 aja anapita ku Galileya,+ kuphiri kumene Yesu anawauza kuti akakumane nawo.+ Maliko 14:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma ndikadzauka kwa akufa, ndidzatsogola kukafika ku Galileya inu musanafikeko.”+