Maliko 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwo atatuluka mʼmandawo anayamba kuthawa akunjenjemera komanso kunthunthumira kwambiri. Ndipo sanauze munthu aliyense zimene zinachitikazo chifukwa anali ndi mantha.*+ Luka 24:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 ndipo anachoka kumandako* nʼkubwerera kukanena zonsezi kwa ophunzira 11 aja ndi kwa ena onse.+
8 Iwo atatuluka mʼmandawo anayamba kuthawa akunjenjemera komanso kunthunthumira kwambiri. Ndipo sanauze munthu aliyense zimene zinachitikazo chifukwa anali ndi mantha.*+